6
Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 Dulani makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku ena a m’Baibulo a Malemba a Chiheberi. Funsani anthu a m’banja mwanu komanso anzanu. Genesis Buku lofotokoza mmene paradaiso anathera Ekisodo Mulungu anapulumutsa anthu ake modabwitsa Levitiko Malamulo a Mulungu anawathandiza kukhala oyera tsiku lililonse Numeri Ena analephera kukalowa m’Dziko Lolonjezedwa KHALANI BWENZI LA YEHOVA ZOCHITA s PINDANI PINDANI www.jw.org 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania Tsamba 1

Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

  • Upload
    others

  • View
    2

  • Download
    0

Embed Size (px)

Citation preview

Page 1: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1Dulani makadiwa kuti akuthandizeni kuloweza mabuku ena a m’Baibulo a Malemba aChiheberi. Funsani anthu a m’banja mwanu komanso anzanu.

GenesisBuku lofotokoza

mmene paradaiso anathera

EkisodoMulungu anapulumutsaanthu ake modabwitsa

LevitikoMalamulo a Mulungu

anawathandiza kukhalaoyera tsiku lililonse

NumeriEna analephera kukalowa

m’Dziko Lolonjezedwa

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 1

Page 2: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

DeuteronomoAnalimbikitsidwa

kuti akhale omvera

YoswaBanja lililonse

linali ndi malo awoawo

OweruzaAnthu a Mulungu

ankachita zinthu zodabwitsa

RuteAnapeza mwamunandiponso pokhala

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 2

Page 3: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

1 SamueliMulungu anasankha

Davide kuti akhale mfumu

2 SamueliM’banja lake munali mavutochifukwa cha machimo ake

1 MafumuUfumu unagawanika,

wina kumpoto wina kumwera

2 MafumuNgakhale kuti

ambiri ankachita zoipa,ochepa anali okhulupirika

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 3

Page 4: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

1 MbiriAnaphunzirapo kathu

pa zochitika zakale

2 MbiriMtunduwo unakumana ndi mavuto

chifukwa cha mafumu oipa.

EzaraAnathandiza kuti anthu

ayambenso kulambira Yehova

NehemiyaAnathandiza kuti mzinda

ndi mpanda wake zimangidwenso

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 4

Page 5: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

EsitereAnayankhula molimba mtima

pa nthawi yoyenera

YobuKukhala wokhulupirika

kumasangalatsa Mulungu

MasalimoNyimbo zotamanda

chikondi cha Mulungu ndimphamvu zake

MiyamboNzeru zopezeka m’mawu ake

n’zothandiza kwambiri

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 5

Page 6: Lowezani Mabuku a M’Baibulo—Gawo 1 · Ezara Anathandiza kuti anthu ayambenso kulambiraYehova Nehemiya Anathandiza kuti mzinda ndi mpanda wake zimangidwenso KHALANI BWENZI LAYEHOVA

MlalikiKutumikira Mulungu

n’kosangalatsa kwambiri

Nyimbo ya SolomoChikondi chenicheni

chimakhalapo nthawi zonse

YesayaMmene moyo udzakhalire

Yesu akadzayamba kulamulira

KHALANI BWENZI LA YEHOVA � ZOCHITA

s

PINDANI

PINDANI

www.jw.org � 2015 Watch Tower Bible and Tract Society of PennsylvaniaTsamba 6